Genesis 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nthawi yomweyo Yosefe anakumbukira maloto ake aja okhudza abale akewo.+ Choncho anawauza kuti: “Inu ndinu akazitape! Mwabwera kuno kudzafufuza malo amene dziko lathu lili lofooka!” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:9 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 13
9 Nthawi yomweyo Yosefe anakumbukira maloto ake aja okhudza abale akewo.+ Choncho anawauza kuti: “Inu ndinu akazitape! Mwabwera kuno kudzafufuza malo amene dziko lathu lili lofooka!”