-
Genesis 42:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Tumani mmodzi wa inu kuti apite kukatenga mngʼono wanuyo. Enanu ndikutsekerani mʼndende. Ndikufuna ndione ngati mukunena zoona. Ndipo ngati si zoona, pali Farao wamoyo, ndiye kuti ndinu akazitape basi.”
-