-
Genesis 42:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno mukabweretse mngʼono wanuyo kwa ine. Mukatero, ndidzatsimikiza kuti mukunena zoona, moti simudzaphedwa.” Iwo anachitadi zomwezo.
-