Genesis 42:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Rubeni anayankha kuti: “Kodi ine sindinakuuzeni kuti, ‘Mwanayu musamuchitire zoipaʼ?* Koma inu simunamvere.+ Si izi nanga, magazi ake akufunidwatu kwa ife.”+
22 Ndiyeno Rubeni anayankha kuti: “Kodi ine sindinakuuzeni kuti, ‘Mwanayu musamuchitire zoipaʼ?* Koma inu simunamvere.+ Si izi nanga, magazi ake akufunidwatu kwa ife.”+