-
Genesis 42:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Pamene ankakhuthula matumba awo, aliyense anapeza kachikwama ka ndalama zake mʼthumba lake. Iwo limodzi ndi bambo awo ataona ndalamazo, anachita mantha.
-