Genesis 42:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma bambowo anati: “Zoti mwana wanga apite nanu, izo ndiye ndakana, chifukwa mʼbale wake anafa, ndipo iye anatsala yekha.+ Ngati ngozi yoopsa itamuchitikira panjira nʼkufa, ndithu mudzatsitsira ku Manda*+ imvi zanga chifukwa cha chisoni.”+
38 Koma bambowo anati: “Zoti mwana wanga apite nanu, izo ndiye ndakana, chifukwa mʼbale wake anafa, ndipo iye anatsala yekha.+ Ngati ngozi yoopsa itamuchitikira panjira nʼkufa, ndithu mudzatsitsira ku Manda*+ imvi zanga chifukwa cha chisoni.”+