Genesis 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Yuda anauza bambo ake kuti: “Munthu ujatu anatichenjeza momveka bwino kuti, ‘Musadzabwerenso kwa ine* pokhapokha mʼbale wanuyo mutabwera naye.’+
3 Koma Yuda anauza bambo ake kuti: “Munthu ujatu anatichenjeza momveka bwino kuti, ‘Musadzabwerenso kwa ine* pokhapokha mʼbale wanuyo mutabwera naye.’+