Genesis 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu Wamphamvuyonse apangitse munthuyo kukuchitirani chifundo, kuti akamasule mʼbale wanu uja, ndipo mukabwere naye limodzi ndi Benjamini. Koma ngati ndingataye ana angawa, chabwino, zikhale choncho!”+
14 Mulungu Wamphamvuyonse apangitse munthuyo kukuchitirani chifundo, kuti akamasule mʼbale wanu uja, ndipo mukabwere naye limodzi ndi Benjamini. Koma ngati ndingataye ana angawa, chabwino, zikhale choncho!”+