Genesis 43:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo mwamunayo anati: “Musachite mantha, simunalakwe chilichonse. Mulungu wanu, Mulungu wa bambo anu ndi amene anaika chumacho mʼmatumba mwanu. Ndalama zanu ndinalandira kale.” Atatero mwamunayo anamasula Simiyoni nʼkumupititsa kwa iwo.+
23 Pamenepo mwamunayo anati: “Musachite mantha, simunalakwe chilichonse. Mulungu wanu, Mulungu wa bambo anu ndi amene anaika chumacho mʼmatumba mwanu. Ndalama zanu ndinalandira kale.” Atatero mwamunayo anamasula Simiyoni nʼkumupititsa kwa iwo.+