Genesis 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yosefe anawafunsa za moyo wawo. Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwanji? Kodi adakali ndi moyo?”+
27 Kenako Yosefe anawafunsa za moyo wawo. Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwanji? Kodi adakali ndi moyo?”+