Genesis 43:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anayankha kuti: “Kapolo wanu bambo athu ali bwino. Adakali ndi moyo.” Atatero anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
28 Iwo anayankha kuti: “Kapolo wanu bambo athu ali bwino. Adakali ndi moyo.” Atatero anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+