Genesis 43:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yosefe anachokapo mofulumira chifukwa anagwidwa chifundo ataona mʼbale wakeyo. Anafunafuna malo oti akalirireko, ndiye analowa mʼchipinda chimene munalibe anthu nʼkugwetsa misozi.+
30 Ndiyeno Yosefe anachokapo mofulumira chifukwa anagwidwa chifundo ataona mʼbale wakeyo. Anafunafuna malo oti akalirireko, ndiye analowa mʼchipinda chimene munalibe anthu nʼkugwetsa misozi.+