Genesis 43:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Abale akewo anawauza kuti akhale pansi pamaso pake, kuyambira wamkulu kwambiri*+ mpaka wamngʼono kwambiri. Iwo ankangoyangʼanana modabwa.
33 Abale akewo anawauza kuti akhale pansi pamaso pake, kuyambira wamkulu kwambiri*+ mpaka wamngʼono kwambiri. Iwo ankangoyangʼanana modabwa.