Genesis 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Kenako Yosefe analamula woyangʼanira nyumba yake uja kuti: “Udzazitse chakudya mʼmatumba a anthuwa chimene angakwanitse kunyamula. Aliyense umubwezere ndalama zake ndipo uziike pakamwa pa thumba lake.+
44 Kenako Yosefe analamula woyangʼanira nyumba yake uja kuti: “Udzazitse chakudya mʼmatumba a anthuwa chimene angakwanitse kunyamula. Aliyense umubwezere ndalama zake ndipo uziike pakamwa pa thumba lake.+