-
Genesis 44:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma uike kapu yanga yasiliva ija pakamwa pa thumba la wamngʼonoyo limodzi ndi ndalama zake zogulira tirigu.” Choncho woyangʼanira nyumba yakeyo anachita zimene Yosefe anamuuzazo.
-