-
Genesis 44:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Iwo asanapite patali kuchokera mumzindawo, Yosefe anauza woyangʼanira nyumba yake kuti: “Nyamuka, athamangire anthu aja. Ukawapeza uwafunse kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani mwabwezera zoipa pa zabwino?
-