Genesis 44:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pajatu ndalama zimene tinazipeza pakamwa pa matumba athu kudziko la Kanani tinazibweza kwa inu.+ Ndiye zingatheke bwanji kuti tibe siliva ndi golide mʼnyumba ya mbuye wanu?
8 Pajatu ndalama zimene tinazipeza pakamwa pa matumba athu kudziko la Kanani tinazibweza kwa inu.+ Ndiye zingatheke bwanji kuti tibe siliva ndi golide mʼnyumba ya mbuye wanu?