-
Genesis 44:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Zitatero, iwo anangʼamba zovala zawo. Kenako aliyense anakwezanso thumba lake pabulu wake nʼkubwerera kumzinda kuja.
-