Genesis 44:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yuda+ ndi abale ake atalowa mʼnyumba ya Yosefe, anamupeza adakali mʼnyumbamo, ndipo iwo anagwada nʼkumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+
14 Yuda+ ndi abale ake atalowa mʼnyumba ya Yosefe, anamupeza adakali mʼnyumbamo, ndipo iwo anagwada nʼkumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+