Genesis 44:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yosefe anati: “Ndiye chiyani mwachitachi? Kodi inu simukudziwa kuti munthu ngati ine ndingathe kudziwa zinthu poombeza maula?”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:15 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 31
15 Yosefe anati: “Ndiye chiyani mwachitachi? Kodi inu simukudziwa kuti munthu ngati ine ndingathe kudziwa zinthu poombeza maula?”+