Genesis 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Yosefe anati: “Sindingachite zimenezo! Amene wapezeka ndi kapu yangayo ndi amene akhale kapolo wanga.+ Enanu mupite kwa bambo anu mwamtendere.”
17 Koma Yosefe anati: “Sindingachite zimenezo! Amene wapezeka ndi kapu yangayo ndi amene akhale kapolo wanga.+ Enanu mupite kwa bambo anu mwamtendere.”