Genesis 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Patapita nthawi bambo athu anatiuza kuti, ‘Pitaninso mukatigulireko kachakudya pangʼono.’+