Genesis 44:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma ife tinati, ‘Sitingathe kupitanso. Ngati mungatilole kutenga mngʼono wathuyu tipitako, chifukwa sitingathe kukaonananso ndi munthuyo pokhapokha ngati mngʼono wathuyu titapita naye.’+
26 Koma ife tinati, ‘Sitingathe kupitanso. Ngati mungatilole kutenga mngʼono wathuyu tipitako, chifukwa sitingathe kukaonananso ndi munthuyo pokhapokha ngati mngʼono wathuyu titapita naye.’+