-
Genesis 44:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Bambo amamʼkonda kwambiri mwanayu ngati mmene amakondera moyo wawo. Choncho ndikakangofika kwa kapolo wanu bambo anga ndilibe mwanayu,
-