Genesis 44:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 iwo nʼkuona kuti mwanayu palibe, basi akafa. Ndithu, akapolo anufe tidzatsitsira ku Manda* imvi za kapolo wanu bambo athu chifukwa cha chisoni.
31 iwo nʼkuona kuti mwanayu palibe, basi akafa. Ndithu, akapolo anufe tidzatsitsira ku Manda* imvi za kapolo wanu bambo athu chifukwa cha chisoni.