Genesis 44:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ine kapolo wanu ndinalonjeza bambo anga kuti moyo wa mwanayu udzakhala mʼmanja mwanga. Ndinalonjeza kuti, ‘Ndikadzalephera kubwera naye kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu bambo anga moyo wanga wonse.’+
32 Ine kapolo wanu ndinalonjeza bambo anga kuti moyo wa mwanayu udzakhala mʼmanja mwanga. Ndinalonjeza kuti, ‘Ndikadzalephera kubwera naye kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu bambo anga moyo wanga wonse.’+