-
Genesis 45:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako Yosefe anauza abale akewo kuti: “Ndine Yosefe! Kodi bambo anga adakali ndi moyo?” Koma abale akewo sanathe kumuyankha chifukwa anali atawasokoneza maganizo.
-