Genesis 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma musadzimvere chisoni kapena kuimbana mlandu kuti munandigulitsa kuno, chifukwa Mulungu ndi amene ananditumiza kuno kuti tikhalebe ndi moyo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:5 Nsanja ya Olonda,1/1/1999, tsa. 30
5 Koma musadzimvere chisoni kapena kuimbana mlandu kuti munandigulitsa kuno, chifukwa Mulungu ndi amene ananditumiza kuno kuti tikhalebe ndi moyo.+