Genesis 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho si inu amene munanditumiza kuno, koma ndi Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala nduna yaikulu ya* Farao, mbuye wa nyumba yake yonse ndiponso wolamulira wa dziko lonse la Iguputo.+
8 Choncho si inu amene munanditumiza kuno, koma ndi Mulungu woona. Anachita zimenezi kuti andiike kukhala nduna yaikulu ya* Farao, mbuye wa nyumba yake yonse ndiponso wolamulira wa dziko lonse la Iguputo.+