Genesis 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzakhala mʼdziko la Goseni+ kuti mudzakhale pafupi ndi ine. Mubwere inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa zanu, ngʼombe zanu ndi zonse zimene muli nazo.
10 Mudzakhala mʼdziko la Goseni+ kuti mudzakhale pafupi ndi ine. Mubwere inuyo, ana anu, adzukulu anu, nkhosa zanu, ngʼombe zanu ndi zonse zimene muli nazo.