Genesis 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneko ndizidzakupatsani chakudya chifukwa kwatsala zaka 5 za njala.+ Mukapanda kuchita zimenezi, inuyo ndi amʼnyumba yanu komanso zonse zimene muli nazo muvutika ndi njala.”’
11 Kumeneko ndizidzakupatsani chakudya chifukwa kwatsala zaka 5 za njala.+ Mukapanda kuchita zimenezi, inuyo ndi amʼnyumba yanu komanso zonse zimene muli nazo muvutika ndi njala.”’