Genesis 45:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inuyo ndi mʼbale wangayu Benjamini, mukuona ndi maso anu kuti ndine amene ndikulankhula nanu.+