-
Genesis 45:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho Farao anauza Yosefe kuti: “Abale akowa uwauze kuti, ‘Chitani izi: Kwezani katundu panyama zanu, mupite kudziko la Kanani.
-