Genesis 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwauzenso kuti:+ ‘Chitani izi: Mutenge ngolo+ kuno ku Iguputo zoti mukatengeremo ana anu ndi akazi anu. Ngolo ina mukatengeremo bambo anu nʼkubwera kuno.+
19 Uwauzenso kuti:+ ‘Chitani izi: Mutenge ngolo+ kuno ku Iguputo zoti mukatengeremo ana anu ndi akazi anu. Ngolo ina mukatengeremo bambo anu nʼkubwera kuno.+