-
Genesis 45:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ana a Isiraeli aja anachitadi zimenezo. Yosefe anawapatsa ngolo monga momwe Farao analamulira. Anawapatsanso chakudya cha pa ulendo.
-