Genesis 45:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Aliyense wa iwo anamupatsa chovala chatsopano, koma Benjamini anamupatsa zovala zatsopano 5, ndi ndalama zasiliva 300.+
22 Aliyense wa iwo anamupatsa chovala chatsopano, koma Benjamini anamupatsa zovala zatsopano 5, ndi ndalama zasiliva 300.+