Genesis 45:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Isiraeli anafuula kuti: “Basi, tsopano ndakhulupirira! Yosefe mwana wanga adakali ndi moyo! Ndipita ndikamuone ndisanafe!”+
28 Kenako Isiraeli anafuula kuti: “Basi, tsopano ndakhulupirira! Yosefe mwana wanga adakali ndi moyo! Ndipita ndikamuone ndisanafe!”+