Genesis 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Choncho Isiraeli anatenga banja lake komanso zinthu zonse zimene anali nazo nʼkunyamuka. Atafika ku Beere-seba+ anapereka nsembe kwa Mulungu wa bambo ake Isaki.+
46 Choncho Isiraeli anatenga banja lake komanso zinthu zonse zimene anali nazo nʼkunyamuka. Atafika ku Beere-seba+ anapereka nsembe kwa Mulungu wa bambo ake Isaki.+