Genesis 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu woona, Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakupangitsa kukhala mtundu waukulu.+
3 Mulungu anamuuza kuti: “Ine ndine Mulungu woona, Mulungu wa bambo ako.+ Usaope kupita ku Iguputo, chifukwa kumeneko ndidzakupangitsa kukhala mtundu waukulu.+