Genesis 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ineyo ndipita nawe ku Iguputo, ndiponso ine ndi amene ndidzabwere nawe mʼdziko lino kuchokera kumeneko.+ Ndipo Yosefe ndi amene adzakutseke maso pa imfa yako.”+
4 Ineyo ndipita nawe ku Iguputo, ndiponso ine ndi amene ndidzabwere nawe mʼdziko lino kuchokera kumeneko.+ Ndipo Yosefe ndi amene adzakutseke maso pa imfa yako.”+