-
Genesis 46:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Yakobo ananyamuka ku Beere-sebako. Ana a Isiraeliwo anatenga Yakobo bambo awo, limodzi ndi ana awo komanso akazi awo. Anawatengera mʼngolo zimene Farao anatumiza.
-