Genesis 46:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awa ndi mayina a ana a Isiraeli, kapena kuti ana a Yakobo, omwe anapita nawo ku Iguputo:+ Mwana woyamba wa Yakobo anali Rubeni.+
8 Awa ndi mayina a ana a Isiraeli, kapena kuti ana a Yakobo, omwe anapita nawo ku Iguputo:+ Mwana woyamba wa Yakobo anali Rubeni.+