Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+
12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+