Genesis 46:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amenewa ndi ana a Leya, amene anaberekera Yakobo ku Padani-aramu, kuphatikizapo Dina+ mwana wamkazi wa Yakobo. Ana onse aamuna ndi aakazi komanso zidzukulu zake analipo 33.
15 Amenewa ndi ana a Leya, amene anaberekera Yakobo ku Padani-aramu, kuphatikizapo Dina+ mwana wamkazi wa Yakobo. Ana onse aamuna ndi aakazi komanso zidzukulu zake analipo 33.