Genesis 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yosefe anauza bambo ake ndi abale akewo kuti azikhala ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino kwambiri adzikolo ku Ramese*+ monga mmene Farao analamulira.
11 Choncho Yosefe anauza bambo ake ndi abale akewo kuti azikhala ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino kwambiri adzikolo ku Ramese*+ monga mmene Farao analamulira.