Genesis 47:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chakudya chinatheratu mʼdziko lonselo ndipo njala inafika poipa kwambiri. Anthu onse a ku Iguputo ndi a ku Kanani anali ofooka chifukwa cha njalayo.+
13 Chakudya chinatheratu mʼdziko lonselo ndipo njala inafika poipa kwambiri. Anthu onse a ku Iguputo ndi a ku Kanani anali ofooka chifukwa cha njalayo.+