Genesis 47:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yosefe anasonkhanitsa ndalama zonse zimene zinali mʼdziko la Iguputo ndi la Kanani, zomwe anthu ankagulira chakudya.+ Iye ankatenga ndalamazo nʼkuzipititsa kunyumba kwa Farao.
14 Yosefe anasonkhanitsa ndalama zonse zimene zinali mʼdziko la Iguputo ndi la Kanani, zomwe anthu ankagulira chakudya.+ Iye ankatenga ndalamazo nʼkuzipititsa kunyumba kwa Farao.