-
Genesis 47:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho anthuwo anayamba kubweretsa ziweto zawo kwa Yosefe. Yosefeyo ankawapatsa chakudya posinthanitsa ndi mahatchi awo, nkhosa, ngʼombe ndi abulu. Mʼchaka chonsecho, Yosefe ankawapatsa chakudya posinthanitsa ndi ziweto zawo.
-