-
Genesis 47:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Yosefe anagulira Farao minda yonse ya Aiguputo, chifukwa munthu aliyense wa mu Iguputo anagulitsa munda wake. Anachita zimenezi chifukwa njala inali itafika poopsa, moti minda yonse inakhala ya Farao.
-