Genesis 47:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Yosefe anakhazikitsa lamulo limene lilipobe mpaka lero lakuti, Farao azilandira gawo limodzi mwa magawo 5 a zokolola za minda yonse ya mu Iguputo. Koma malo a ansembe okha sanakhale a Farao.+
26 Choncho Yosefe anakhazikitsa lamulo limene lilipobe mpaka lero lakuti, Farao azilandira gawo limodzi mwa magawo 5 a zokolola za minda yonse ya mu Iguputo. Koma malo a ansembe okha sanakhale a Farao.+